CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
’Madalitso Onsewa . . . Adzakupeza’
Anthu onse amene amamvera mawu a Yehova amalandira madalitso ambiri (De 28:1, 3-6; w10 12/15 19 ¶18)
Atumiki okhulupirika a Yehova adzapeza madalitso (De 28:2; w01 9/15 10 ¶2)
Yehova amafuna kuti tizichita zomwe amafuna ‘mokondwera, komanso ndi mtima wosangalala’ (De 28:45-47; w10 9/15 8 ¶4)
Atumiki a Yehova okhulupirika akusangalala ndi madalitso ambiri panopa, ndipo m’tsogolomu adzapeza madalitso enanso amene Yehova analonjeza.