Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 8
  • Musamaone Zinthu Zopanda Pake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Musamaone Zinthu Zopanda Pake
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • ‘Madalitso Onsewa . . . Adzakupeza’
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Anachita Pangano ndi Davide
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mbala mu Israyeli
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 8
Zithunzi: 1. Akani akuba zinthu. 2. M’bale akuonera zinthu zosayenera pa kompyuta yake usiku.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Musamaone Zinthu Zopanda Pake

Maso a Akani anamuchititsa kuti atenge zinthu zomwe sizinali zake (Yos 7:1, 20, 21; w10 4/15 20 ¶5)

Zochita za Akani zinakhudza banja lake komanso mtundu wonse wa Aisiraeli (Yos 7:4, 5, 24-26; w97 8/15 28 ¶2)

Tizikhala odziletsa (1Yo 2:15-17; w10 4/15 21 ¶8)

Tizipewa zinthu zopanda pake zimene sizidzapezeka m’dziko latsopano lomwe mudzakhale chilungamo.​—2Pe 3:13.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena