Ekisodo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa makolo* ako, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Atatero Mose anaphimba nkhope yake chifukwa ankaopa kuyangʼana Mulungu woona. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,5/1/2005, tsa. 13
6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa makolo* ako, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Atatero Mose anaphimba nkhope yake chifukwa ankaopa kuyangʼana Mulungu woona.