-
Ekisodo 34:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Poyankha Mulungu anati: “Ine ndikuchita nanu pangano ili: Ndidzachita zinthu zodabwitsa pamaso pa anthu ako onse, zimene sizinachitikepo padziko lonse lapansi kapena pakati pa mitundu yonse.+ Ndipo anthu onse okuzungulirani adzaonadi ntchito za Yehova, chifukwa ndidzakuchitirani chinthu chochititsa mantha.+
-