Ekisodo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* ndi wanga,+ kuphatikizapo mwana woyamba kubadwa wa ziweto zanu zonse, kaya ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena nkhosa.+
19 Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* ndi wanga,+ kuphatikizapo mwana woyamba kubadwa wa ziweto zanu zonse, kaya ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena nkhosa.+