Numeri 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mbadwa za Simiyoni,+ anazilemba mayina mmodzi ndi mmodzi. Anazilemba mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
22 Mbadwa za Simiyoni,+ anazilemba mayina mmodzi ndi mmodzi. Anazilemba mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.