Numeri 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mbadwa za Simiyoni,+ anazilemba mayina mmodzi ndi mmodzi. Anazilemba malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba amuna onse kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.
22 Mbadwa za Simiyoni,+ anazilemba mayina mmodzi ndi mmodzi. Anazilemba malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba amuna onse kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.