Numeri 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mbadwa za Isakara,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
28 Mbadwa za Isakara,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.