Numeri 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mbadwa za Isakara,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.
28 Mbadwa za Isakara,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.