Numeri 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mbadwa za Nafitali,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
42 Mbadwa za Nafitali,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.