Numeri 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mbadwa za Nafitali,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.
42 Mbadwa za Nafitali,+ anazilemba mayina malinga ndi mabanja awo, ndiponso potsata nyumba za makolo awo. Analemba kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, aliyense woyenerera kupita kunkhondo.