1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 16
19 Kenako anadzuka m’mawa kwambiri n’kugwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi pamaso pa Yehova. Atatero anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona+ ndi mkazi wake Hana, ndipo Yehova anayamba kum’kumbukira.+