Yobu 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+
13 Madalitso+ a munthu amene watsala pang’ono kuwonongedwa ankabwera kwa ine,Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+