Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa Yehova amakonda chilungamo,Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [Ayin] Adzawateteza nthawi zonse.+Koma mbadwa za anthu oipa zidzaphedwa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:28 Yandikirani, ptsa. 285-288 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, tsa. 19
28 Chifukwa Yehova amakonda chilungamo,Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [Ayin] Adzawateteza nthawi zonse.+Koma mbadwa za anthu oipa zidzaphedwa.+