Salimo 65:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mudzatiyankha pochita zinthu zachilungamo zomwe ndi zochititsa mantha,+Inu Mulungu amene mumatipulumutsa.Anthu amene amakhala kumbali zonse za dziko lapansi amakudalirani+Kuphatikizapo amene amakhala kutali, kutsidya la nyanja.
5 Mudzatiyankha pochita zinthu zachilungamo zomwe ndi zochititsa mantha,+Inu Mulungu amene mumatipulumutsa.Anthu amene amakhala kumbali zonse za dziko lapansi amakudalirani+Kuphatikizapo amene amakhala kutali, kutsidya la nyanja.