Salimo 125:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, anthu abwino muwachitire zabwino,+Muchitire zabwino anthu owongoka mtima.+