Yesaya 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakhala atawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Adalitsike Aiguputo anthu anga, Asuri ntchito ya manja anga komanso Aisiraeli omwe ndi cholowa changa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Yesaya 1, ptsa. 206-207
25 chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakhala atawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Adalitsike Aiguputo anthu anga, Asuri ntchito ya manja anga komanso Aisiraeli omwe ndi cholowa changa.”+