Yesaya 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 popeza Yehova wa makamu adzawadalitsa+ n’kuwauza kuti: “Adalitsike Aiguputo anthu anga, Asuri+ ntchito ya manja anga, ndi Aisiraeli cholowa changa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:25 Yesaya 1, ptsa. 206-207
25 popeza Yehova wa makamu adzawadalitsa+ n’kuwauza kuti: “Adalitsike Aiguputo anthu anga, Asuri+ ntchito ya manja anga, ndi Aisiraeli cholowa changa.”+