Yesaya 45:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ineyo ndinapanga dziko lapansi+ ndipo ndinalenga munthu nʼkumuika padzikolo.+ Ndinatambasula kumwamba ndi manja angawa,+Ndipo zinthu zonse zimene zili kumwambako* ndimazipatsa malamulo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:12 Yesaya 2, ptsa. 85-86
12 Ineyo ndinapanga dziko lapansi+ ndipo ndinalenga munthu nʼkumuika padzikolo.+ Ndinatambasula kumwamba ndi manja angawa,+Ndipo zinthu zonse zimene zili kumwambako* ndimazipatsa malamulo.+