Yesaya 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mwamva komanso kuona zonsezo. Kodi simudzauza ena zimenezi?+ Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndikulengeza zinthu zatsopano kwa inu,+Zinsinsi zobisika zimene simunkazidziwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:6 Yesaya 2, ptsa. 123-125
6 Inuyo mwamva komanso kuona zonsezo. Kodi simudzauza ena zimenezi?+ Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndikulengeza zinthu zatsopano kwa inu,+Zinsinsi zobisika zimene simunkazidziwa.