Yesaya 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mwazimva.+ Onani zonsezo.+ Kodi simudzazifotokozera ena?+ Kuyambira panopa ine ndikukuuzani zinthu zatsopano. Ndakuuzani zinthu zobisika zimene simunali kuzidziwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:6 Yesaya 2, ptsa. 123-125
6 Inuyo mwazimva.+ Onani zonsezo.+ Kodi simudzazifotokozera ena?+ Kuyambira panopa ine ndikukuuzani zinthu zatsopano. Ndakuuzani zinthu zobisika zimene simunali kuzidziwa.+