Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa nthawi yonse imene iwo ankavutika, iye ankavutikanso.+ Ndipo mthenga wake* anawapulumutsa.+ Iye anawawombola chifukwa cha chikondi komanso chifundo chake,+Ndipo nthawi zonse ankawakweza mʼmwamba komanso kuwanyamula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2018, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 354-356
9 Pa nthawi yonse imene iwo ankavutika, iye ankavutikanso.+ Ndipo mthenga wake* anawapulumutsa.+ Iye anawawombola chifukwa cha chikondi komanso chifundo chake,+Ndipo nthawi zonse ankawakweza mʼmwamba komanso kuwanyamula.+
63:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2018, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 354-356