Danieli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 mpaka pamene Wamasiku Ambiri+ anabwera ndipo anapereka chiweruzo chokomera oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ndipo nthawi yomwe inaikidwiratu yoti oyerawo atenge ufumu inakwana.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:22 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,2/1/1998, ptsa. 17-18
22 mpaka pamene Wamasiku Ambiri+ anabwera ndipo anapereka chiweruzo chokomera oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ndipo nthawi yomwe inaikidwiratu yoti oyerawo atenge ufumu inakwana.+