Danieli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba yachifumu* ku Susani,+ imene ili mʼchigawo cha Elamu.+ Ndinaona masomphenyawa kuti ndinali mʼmphepete mwa mtsinje wa Ulai. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 Ulosi wa Danieli, ptsa. 165-166
2 Ndikuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba yachifumu* ku Susani,+ imene ili mʼchigawo cha Elamu.+ Ndinaona masomphenyawa kuti ndinali mʼmphepete mwa mtsinje wa Ulai.