Danieli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:19 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, tsa. 184
19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+