Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 79:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+

      Tisonyezeni chifundo chanu mofulumira,+

      Chifukwa zativuta kwambiri.

       9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+

      Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.

      Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+

  • Yesaya 63:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Dzikoli linali la anthu anu oyera kwa kanthawi kochepa.

      Koma adani athu apondaponda malo anu opatulika.+

      19 Kwa nthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo,

      Ngati anthu amene sanadziwikepo ndi dzina lanu.

  • Yeremiya 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Nʼchifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wothedwa nzeru,

      Ndiponso ngati munthu wamphamvu amene sangathe kupulumutsa anthu ake?

      Komatu inu Yehova muli pakati pathu,+

      Ndipo ife timadziwika ndi dzina lanu.+

      Musatisiye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena