Hagai 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzagonjetsa maufumu ndi kuchotsa mphamvu za maufumu a anthu a mitundu ina.+ Ndidzawononga magaleta* ndi okwera pamagaletawo. Mahatchi* ndi okwera pamahatchiwo adzaphedwa ndipo aliyense adzaphedwa ndi mʼbale wake ndi lupanga.’”+ Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Nsanja ya Olonda,12/1/2007, tsa. 94/15/2006, ptsa. 20, 241/1/1997, tsa. 22
22 Ndidzagonjetsa maufumu ndi kuchotsa mphamvu za maufumu a anthu a mitundu ina.+ Ndidzawononga magaleta* ndi okwera pamagaletawo. Mahatchi* ndi okwera pamahatchiwo adzaphedwa ndipo aliyense adzaphedwa ndi mʼbale wake ndi lupanga.’”+