Malaki 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova ankalankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu nʼkumamvetsera. Buku la chikumbutso, lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene ankaganizira za dzina lake,* linayamba kulembedwa pamaso pake.+ Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2022, tsa. 144/2022, ptsa. 5-6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 36 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 23-24, 26 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 1112/15/2007, tsa. 295/1/2002, tsa. 224/15/1995, ptsa. 19-2011/1/1993, ptsa. 4-512/1/1992, tsa. 179/1/1987, tsa. 29 Tsiku la Yehova, ptsa. 184-186
16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova ankalankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu nʼkumamvetsera. Buku la chikumbutso, lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene ankaganizira za dzina lake,* linayamba kulembedwa pamaso pake.+
3:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2022, tsa. 144/2022, ptsa. 5-6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 36 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 23-24, 26 Nsanja ya Olonda,12/1/2012, tsa. 1112/15/2007, tsa. 295/1/2002, tsa. 224/15/1995, ptsa. 19-2011/1/1993, ptsa. 4-512/1/1992, tsa. 179/1/1987, tsa. 29 Tsiku la Yehova, ptsa. 184-186