Mateyu 13:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika mʼmunda, chimene munthu anachipeza nʼkuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa zinthu zonse zimene anali nazo nʼkukagula mundawo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:44 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 110-111 Nsanja ya Olonda,12/15/2014, tsa. 104/15/1987, ptsa. 8-9 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 65-66
44 Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika mʼmunda, chimene munthu anachipeza nʼkuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa zinthu zonse zimene anali nazo nʼkukagula mundawo.+
13:44 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 110-111 Nsanja ya Olonda,12/15/2014, tsa. 104/15/1987, ptsa. 8-9 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 65-66