Luka 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lolumala.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 78
6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lolumala.+