Aroma 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amalimbikitsa, azilimbikitsa.+ Wogawa, azigawa mowolowa manja.+ Wotsogolera, azitsogolera mwakhama.+ Ndipo wosonyeza chifundo, azichita zimenezo mosangalala.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 24-25 Nsanja ya Olonda,5/15/1993, ptsa. 19-20
8 Amene amalimbikitsa, azilimbikitsa.+ Wogawa, azigawa mowolowa manja.+ Wotsogolera, azitsogolera mwakhama.+ Ndipo wosonyeza chifundo, azichita zimenezo mosangalala.+