Aroma 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wochenjeza, aike mtima wake pa kuchenjeza.+ Wogawa, agawe mowolowa manja.+ Wotsogolera,+ atsogolere mwakhama. Ndipo wosonyeza chifundo,+ achite zimenezo mokondwa. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 24-25 Nsanja ya Olonda,5/15/1993, ptsa. 19-20
8 Wochenjeza, aike mtima wake pa kuchenjeza.+ Wogawa, agawe mowolowa manja.+ Wotsogolera,+ atsogolere mwakhama. Ndipo wosonyeza chifundo,+ achite zimenezo mokondwa.