1 Akorinto 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo!
15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo!