1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 195
9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.