Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+ Genesis 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini,+ Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wachikanani. Numeri 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai. Numeri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana aamuna a Simiyoni+ mwa mabanja awo anali awa: Nemueli+ amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini+ amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini+ amene anali kholo la banja la Ayakini,
33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+
10 Ana a Simiyoni+ anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini,+ Zohari ndi Shauli+ mwana wa mkazi wachikanani.
12 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai.
12 Ana aamuna a Simiyoni+ mwa mabanja awo anali awa: Nemueli+ amene anali kholo la banja la Anemueli, Yamini+ amene anali kholo la banja la Ayamini, Yakini+ amene anali kholo la banja la Ayakini,