Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,3/1/1995, tsa. 16
4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+