Deuteronomo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti thanthwe lawo silofanana ndi Thanthwe lathu,+Ndipo adani athu angavomereze zimenezi.+