1 Samueli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musachititse kapolo wanu wamkazi kukhala ngati mkazi wopanda pake,+ popeza ndikulankhulabe mpaka pano chifukwa cha kuchuluka kwa nkhawa ndi nsautso.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,2/1/2001, ptsa. 20-21
16 Musachititse kapolo wanu wamkazi kukhala ngati mkazi wopanda pake,+ popeza ndikulankhulabe mpaka pano chifukwa cha kuchuluka kwa nkhawa ndi nsautso.”+