1 Samueli 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwanayo atangosiya kuyamwa, Hana anapita naye ku Silo atatenga ng’ombe yaing’ono yamphongo yazaka zitatu, ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mtsuko waukulu wa vinyo.+ Iye analowa m’nyumba ya Yehova ku Silo,+ ndipo mwanayo anali naye limodzi.
24 Mwanayo atangosiya kuyamwa, Hana anapita naye ku Silo atatenga ng’ombe yaing’ono yamphongo yazaka zitatu, ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mtsuko waukulu wa vinyo.+ Iye analowa m’nyumba ya Yehova ku Silo,+ ndipo mwanayo anali naye limodzi.