2 Samueli 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu Mulungu woona. Kunena za mawu anu, akhale oona,+ pakuti mwandilonjeza ine mtumiki wanu zabwino zimenezi.+
28 Tsopano inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu Mulungu woona. Kunena za mawu anu, akhale oona,+ pakuti mwandilonjeza ine mtumiki wanu zabwino zimenezi.+