Salimo 60:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+ Salimo 118:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+Kusiyana ndi kudalira munthu wochokera kufumbi.+ Salimo 146:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+ Yesaya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+ Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+
11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+
3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+
22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+