Nehemiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno ndinauzanso mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, lolani kuti ndipatsidwe makalata+ okasonyeza kwa abwanamkubwa+ a tsidya lina la Mtsinje,*+ kuti akandilole kudutsa ndi kukafika ku Yuda.
7 Ndiyeno ndinauzanso mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, lolani kuti ndipatsidwe makalata+ okasonyeza kwa abwanamkubwa+ a tsidya lina la Mtsinje,*+ kuti akandilole kudutsa ndi kukafika ku Yuda.