Yobu 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+
16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+