Yobu 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinkawasankhira njira, ndipo ndinkakhala pansi patsogolo pawo.Ndinali ngati mfumu pakati pa asilikali ake,+Ndiponso ngati wotonthoza olira.+
25 Ndinkawasankhira njira, ndipo ndinkakhala pansi patsogolo pawo.Ndinali ngati mfumu pakati pa asilikali ake,+Ndiponso ngati wotonthoza olira.+