Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+