Salimo 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu amene Mulungu akuwadalitsa adzalandira dziko lapansi,+Koma amene wawatemberera adzaphedwa.+