Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:39 Nsanja ya Olonda,8/15/2004, ptsa. 17-18
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+