Salimo 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:6 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, ptsa. 11-12
6 Taonani! Mumakondwera ndi choonadi chochokera pansi pa mtima.+Ndipo mundidziwitse nzeru mumtima mwanga.+