Salimo 74:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+
18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+