Salimo 145:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 145:21 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 209/15/1990, tsa. 20
21 Pakamwa panga padzalankhula zotamanda Yehova,+Ndipo anthu onse atamande dzina lake loyera mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+